NEEM NDI MTENGO OMWE MULUNGU ANAUDALITSA NDI MACHILITSO AMATENDA OSIYANASIYANA.

⚫ NEEM / MKINA

◾Nimu ndi mtengo omwe umawawa kwambiri, Masamba a mtengowo mutha kuwagaya mu Brenda kupanga powder ( ufa) , ma tablet, ma capsules ndi mafuta ( oil) Nimu umachiza pafupifupi nthenda ina iliyonse.

⚫ NJIRA ZACHILENGEDWE

◾Ngati mungamagwiritse ntchito masamba a mtengo wa Neem simungakhala pa chiophyezo chodwala matenda a Cancer.

◾Ngati mwatenga matenda opasirana kudzela munjira yogonana musachedwe, imwani Neem akuthandizani mwansanga, Ngati mukudzimbidwa kapena kukula mimba Tengani masamba a Neem muzimwa. 

◾Ngati mukuvutika ndi thenda ya mtima Tengani masamba a Neem muzimwa.

◾Ngati mumadwala malungo pafupi pafupi kapena mumangomva kudzidzira nthawi zambiri imwani masamba a Neem.

◾ Ngati munagonana ndi okondedwa Anu masiku oti mutha kutenga m'mimba Mukhoza kugwirisa ntchito Neem ngati emergency pill kuti musatenge mimba mukamariza kumenya game.

◾Kwa omwe mukuvutika ndi matenda a sugar, Neem amathandiza kutsitsa sugar wa mthupi mwanu ngati akukwela(Diabetes).

◾Ngati mumavutika ndi matenda a mu usinini imwani Neem.

◾Mukhoza kugwirisa ntchito Neem ngati mukufuna kutsuka mthupi mwanu. 

◾ Ngati muli ndi matenda a mu Liver gwiritsani ntchito masamba a Neem pafupi pafupi.

◾Kwa omwe mukuvutika ndi Fungus Neem amathandiza kuthana ndi fungus.

◾Neem amathandiza kuonjezera chitetezo cha mthupi. 

◾Kwa amene mukuvutika ndi ziphuphu kumaso pezani Neem mudzipaka kapen kumwa.

◾Ngati nthupi lanu limaturutsa fungo, gwiritsani ntchito masamba a Neem wilitsani pamodzi ndi madzi anu osamba.

◾Kwa amene muli ndi mfundu mmutu tengani masamba a Neem ndi kusinja kuwilitsa madziwo Kutsukira mmutu

◾Kwa amene akumva kuyabwa mthupi or mwatuluka mwanabele kapena zidzolo pezani masamba a Neem wilitsani pamodzi ndi madzi anu osamba, ndikusamba madzi amenewo.

◾Kwa Omwe muli ndi vuto la HIV pezani Neemu Muzimwa pafupi pafupi mwachitsomo cha Mulungu mudzapeza MACHILITSO.

◾Neem amachiza matenda ochuluka ena mwa matenda sindinalembe chofunika ndikupeza masamba a Neem mukhale nawo nyumba kapena Muzimwa pafupi pafupi Ngati muli nawo.


⚫ Kwa omwe mukufuna Neem/Mkina powder kapena ufa wa Neem ndipange check WhatsApp number:

+255745469984 

+255737101244

Tikutumizirani Kuli Konse Komwe Muli.


Comments