PHINDU KAPENA DZODABWITSA ZA MCHERE WA MIYALA NDI SABOLA WA MTALI.

 PHINDU KAPENA DZODABWITSA ZA MCHERE WA MIYALA NDI SABOLA WA MTALI.

Tengani mchere wa miyala kapena wa miburu ndi tsabola wamtalimtali ngati yemwe ukuwoneka pachithunzichi kenako sinjani muntondo zonse pakamodzi kenako tengani ka nsalu koyera ndikukulunga mu nsaluko, ndikuyika m'thumba lanu la chovala kapena mu bagi yanu olo kuika mu nsapato yanu mudzapeza zotsatira izi.

1. Mukapita kukafunsira ntchito, muipeza mosavuta. 

2. Mukapita kukapempha thandizo kulikonse mudzapeza kapena kupatsidwa thandizo mosavuta.

 3. Mukapita kwa munthu amene munamungongodza ndalama amavuta kupeleka ngongole, adzakupatsani ndalama zanu nthawi yomweyo. 

4. Anthu onse omwe amakudani kepena kudana nanu akakuonani azayamba kusangalala nanu akakuonani. 

5. Anthu omwe anakuiwalani adzakukumbukirani ndi kukuyamikirani mudzakhala munthu wamwayi palipotse pomwe mungapite. 

Takulandilani ku website yathu mukhoza kupanga advertise business yanu pa mtengo wotsika ndipo advert yanu idzaoneka pa website ya Google. 

W


hat'sapp us: +255737101244

Comments