MUNGADZIWE BWANJI KUTI NDINU OBELEKA KAPENA OSABELEKA

1. MAMUNA

◾Tengani umuna wanu ndikuuika pa msalu yabwino yochapidwa ya cotton kapena tissue, mukatero ikani umuna wanu pakamsalu kenako kapindeni, dikilani 5 minutes, mukaona kuti yamatana pamenepo umuna wanu ndi wamoyo mukhoza kupeleka mimba.

◾Tengani madzi mu tambula kapena mu mkapu ndikuikamo umuna wanu, ngati umuna wanu wamila dziwani kuti ndinu obeleka mutha kupeleka mimba, koma ukayandama pamwamba pa madzi dziwanini kuti sizili bwino pamenepo.


2. MKAZI

◾Ngati period yanu m'mapanga bwino bwino yokhazikika ma date

◾Ngati mmakhala ndi chilakolako chofuna MAMUNA

◾Ngati mukagwilidwa ndi MAMUNA mmava thupi lanu kuti mwagwilidwa ndi MAMUNA

◾Ngati mukamagonana ndi MAMUNA mmava bwino kuti mukugonedwa

◾Ngati thupi lanu m'maliva kuti mukuyandikila kupanga period


◾Ngati izi zonse zilibwino pamoyo wanu ziwani kuti chilichotse chili bwino, kwangotsala ndikutenga mimba.


◾NOTE: Palibe munthu analengedwa ndi Mulungu Ali OSABELEKA.


Comments