◾Soursop ndi mtengo wazipatso omwe Mulungu adaupasanso machiritso amatenda osiyanasiyana.Mphamvu zomwe zili mu masamba amtengo umenewa zimapha cancer cells komanso kuchidza matenda amenewa mopanda zovuta komanso mwachangu.
ENA MWAMATENGA OMWE AMACHIDZA NDIMONGA
1. DIABETES OR SUGAR
◾Masamba a soursop amathandiza kwa anthu omwe amadwala sugar kubwelera mmalo mwake.
2. KUWAWA KWA NSANA
◾Kupweteka kwa nsana masiku ano ndiyo nthenda yomwe ili mkamwa mkamwa ndipo kubwila mankhwala achipatala kukhodza kuyambitsa mavuto ena pomwe masamba a soursop Mulungu adawapasa mphamvu yochidza matendawa popanda kuyambitsa zina nthupi.
3. NYAMAKADZI ILIYONSE
◾Nyamakazi ndimatenda omwe amagwila kwambiri azigogo athu koma pano aliyense ikumuzunguza chifukwa chazovuta zina ndipo masamba a soursop ndi mankhwala ake.
4. URIC ACID
◾Ngati tili ndi vuto la acid kuti wagwila pena pake mnthupi lathu, Masamba a soursop amathandiza kuchotsa Acid thupi
5. KUPANGA BOOST IMMUNE SYSTEM
◾Pedzani masamba a soursop amathandiza kupanga booster immune system yanu.
6. KUSISA HIGH BLOOD PRESSURE
◾Ngati bp yanu yakwela pedzani masamba asoursop ndimawilitsa ndikumamwa madzi ake ndipo bp yanu izatsika kufika pa low penimpeni.
7. FEVER
◾Ngati tavutika ndi fever masamba a soursop ndi mankhwala.
8. KUTUPA KULI KONSE KWAZIWALO.
◾Fufudzani komwe kuli masamba a soursop mkumamwa.
9. KUFEWESA THUPI
◾Mukufuna ka nkhungu kanu kakhale kofewa kapena kosalala, ndikopanda mabampu?. Pezani komwe kuli masamba a soursop muzigwilisa ntchito kumawilitsa mdikumamwa.
10. KUSAMALA TSITSI
◾Ngati muli ndi tsitsi longonyolozoka ngati la mphaka, gwiritsani ntchito masamba a soursop mowilikiza ndipo tsitsi lanu lidzakhala la mzindo
⚫ KAPANGIDWE KAKE
1. NJIRA YOYAMBA
◾Pezani masamba a soursop a fresh ochulukilapo aikeni mu ntondo ndikusinja kenako aikeni pa saka losukidwa bwino ndi kufinya mupeze 1 glass ndipo sakanizani ndi 1 and half glass ya madzi a ginger, kenako ndipo Thilani 3 teaspoons ya uchi wa original ndikutakasa bwino lomwe.
◾ Kenako mpatseni odwala azimwa 3 teaspoons tsiku lilirotse kwamasiku 14 kapena 21 days. ndipo kwa odwala nyamakadzi azitenga madziwo ndikumatikitila pamalo pomwe pakukupweteka.
⚫ YACHIWIRI
◾Wilitsani masamba a soursop limodzi ndi ginger kenako Phulani ndikutenga madzi okhawo. Ndikumamwa maziwo 50 mils tsiku lilirotse kwamasiku 14 kapena 21
.jpeg)
Comments
Post a Comment